Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2022 la Mboni za Yehova Padziko Lonse

Onani mmene ntchito yolalikira yomwe a Mboni za Yehova amagwira yayendera padziko lonse kuchokera mu September 2021 mpaka mu August 2022.

Ziwerengero Zonse za 2022

Lipoti la pachakali likusonyeza khama limene a Mboni za Yehova amachita komanso ndalama zimene anagwiritsa ntchito pa ntchito yolalikira padziko lonse.

Lipoti la Mayiko Komanso Madera la 2022

Lipotili likuphatikizaponso chiwerengero cha a Mboni, obatizidwa, opezeka pa Chikumbutso ndi zinanso.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.

Mavidiyo Othandiza Muutumiki

Kodi a Mboni za Yehova ndi Anthu Otani?

Anthu ambiri amafuna atadziwa kuti a Mboni za Yehova ndi anthu otani. Onerani vidiyoyi kuti akuuzeni okha zimene amakhulupirira.

ZOKHUDZA IFEYO

Mboni za Yehova padziko lonse

Werengani kuti mudziwe mmene a Mboni za Yehova alili ogwirizana padziko lonse.

ZOKHUDZA IFEYO

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.