GALAMUKANI! Na. 6 2016 | Kodi Tingapewe Bwanji Matenda?

Matenda akale komanso amene angoyamba kumene akhoza kusokoneza thanzi lanu. Kodi mungadziteteze bwanji?

NKHANI YAPACHIKUTO

Kodi Tingapewe Bwanji Matenda?

Tsiku lililonse thupi lanu limamenya nkhondo yolimbana ndi adani osaoneka koma oopsa kwambiri.

NKHANI YAPACHIKUTO

Dzitetezeni ku Matenda

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 5 zimene zingayambitse matenda ndiponso mmene mungadzitetezere.

KODI ZINANGOCHITIKA ZOKHA?

Ulusi wa Nkhono Yam’madzi

Nkhono zinazake zam’madzi zimamata kuzinthu pogwiritsa ntchito timaulusi. Kumvetsa mmene zimenezi zimathekera kungathandize anthu kupeza njira yabwino yomatira zinthu pakhoma kapena yolumikizira minyewa kumafupa.

MFUNDO ZOTHANDIZA MABANJA

Kodi Mungasonyezane Bwanji Ulemu?

Anthu okwatirana ayenera kusonyezana ulemu nthawi zonse. Koma kodi inuyo mungasonyeze bwanji kuti mumalemekeza mwamuna kapena mkazi wanu?

TIONE ZAKALE

Desiderius Erasmus

Munthu wina ananena kuti Erasmus anali wotchuka mofanana ndi mmene zilili ndi anthu ena amene ndi otchuka padziko lonse masiku ano. Kodi n’chiyani chinam’pangitsa kutchuka chonchi?

Nsomba Yochititsa Chidwi Kwambiri

Nsombayi ndi yaing’ono koma yokongola kwambiri komanso imakhala pakati pa nyama zinazake zapoizoni. Kodi zimenezi zimatheka bwanji?

ZIMENE BAIBULO LIMANENA

Kusunga Nthawi

Zimene mumachita pa nkhani yosunga nthawi zingapangitse kuti mukhale ndi mbiri yabwino kapena ayi. Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhaniyi? Nanga mungatani kuti muzitha kuchita zinthu pa nthawi yake?

Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2016

Mndandanda wa nkhani za m’magazini a 2016.

Zina zimene zili pawebusaiti

Uzikhala Waukhondo

Yehova amaika chilichonse pamalo oyenera. Onani zimene nanunso mungachite kuti muzikhala aukhondo

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Khirisimasi?

Mukhoza kudabwa mutadziwa mbiri ya miyambo 6 imene imachitika pa Khirisimasi