Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:

Kodi Munayamba Mwadzifunsapo Kuti:
  • N’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri chonchi?

  • Kodi mungapeze kuti nzeru zokuthandizani kulimbana ndi mavuto?

  • Kodi Mulungu amasamala za inuyo panokha?​—1 Petulo 5:6, 7.

  • Kodi mungadziwe bwanji zokhudza Mulungu ndi zimene amafuna?

Anthu mamiliyoni ambiri apeza mayankho othandiza a mafunso amenewa pophunzira Malemba Opatulika. Nanunso mukhoza kupeza mayankho a mafunsowa.

Ngati mukufuna kumva zambiri, pemphani amene amafalitsa magaziniyi kuti akupatseni kwaulere kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu kapenanso werengani kabukuka pa www.mr1310.com.