Khalani Bwenzi la Yehova (nyimbo zina)

Muzikonda Anthu a Mitundu Yonse

N’chifukwa chiyani kukonda anthu a mitundu yonse n’kofunika kwambiri?

Muzilemekeza Akuluakulu

Kodi mungasonyeze bwanji kuti mumalemekeza Akhristu okalamba amene atumikira Yehova kwa zaka zambiri?

Lowezani Mabuku a M’Baibulo (Gawo 1)

Dziwani ndondomeko ya mabuku a M’malemba Achiheberi kuyambira Genesis mpaka Yesaya.

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—(Gawo 2)

Lowezani mabuku a Malemba Achiheberi m’ndondomeko yake kuyambira Yeremiya mpaka Malaki.

Uzithokoza

Kodi mungayamikire bwanji anthu amene akuchitirani zabwino?

Lowezani Mabuku a M’Baibulo (Gawo 3)

Dziwani ndondomeko ya mabuku a M’malemba Achigiriki Achikhristu kuyambira Mateyu mpaka Chivumbulutso.

Moyo wa Yesu

Kodi Yesu anachita zinthu ziti ali padziko lapansi, nanga posachedwapa adzachita chiyani?

Uzipempherera Ena

N’chifukwa chiyani muyenera kupempherera ena?

Ndakonzekera Kuchita Zambiri

Kodi zolinga zako zauzimu ndi zotani?

Ndinalengedwa Modabwitsa

Mutha kuona, kumva, kuseka, ndi kusewera chifukwa munalengedwa modabwitsa.

Yehova Ndi Mnzanga Wapamtima

Sankhani Mulungu kuti akhale Bwenzi lanu lapamtima!

Timakonda Kulambira kwa Pabanja

Kulambira kwa Pabanja kudzakuthandizani kuti muyandikire kwambiri Yehova.

Ili ndi Banja Lathu

Imbani nyimbo yosonyeza kuti mumakonda banja lanu.

Zikomo Kuti Ndinu Mnzanga

Muzikonda anthu ena ndipo azikhala anzanu apamtima!

Uzikhala Wokhulupirika

Kodi ungatani kuti ukhalebe wokhulupirika?

Esitere Anali Wolimba Mtima

Esitere anachita zinthu zomwe zinali zoyenera​—Inunso mungathe kuchita zoyenera

Chikondi cha Mulungu

Tizitsanzira Mulungu ndi Yesu pokonda anthu onse nthawi zonse.

Mariya—Anali Wodzichepetsa ndi Wololera

Kodi Yehova anagwiritsa ntchito bwanji mtumiki wokhulupirika Mariya? Mvetserani nyimbo yosangalatsa imeneyi ndipo mutsanzira makhalidwe abwino omwe Mariya anali nawo.