Mboni za Yehova Padziko Lonse

Marshall Islands

  • Mudzi wa Laura, Majuro Atoll, Marshall Islands​—Akulalikira m’chinenero cha Chimashalizi kwa munthu woumitsa mtedza wa kokonati

Mfundo Zachidule—Marshall Islands

  • 61,000—Chiwerengero cha anthu
  • 138—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4—Mipingo
  • Pa anthu 496 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Micronesia

Anthu ochokera kumayiko ena amene akutumikira kuzilumba za m’nyanja ya Pacific zimenezi nthawi zambiri amakumana ndi mavuto atatu. Kodi amathana nawo bwanji?