Mboni za Yehova Padziko Lonse

Myanmar

  • Tha Bawt Ngu, Myanmar—Akugawira mabuku othandiza kuphunzira Baibulo

Mfundo Zachidule—Myanmar

  • 56,145,000—Chiwerengero cha anthu
  • 5,171—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 96—Mipingo
  • Pa anthu 10,962 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Myanmar

Kodi n’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova ambiri achoka kwawo kuti akathandize pa ntchito yolalikira ku Myanmar?