Mboni za Yehova Padziko Lonse

Madeira

Mfundo Zachidule—Madeira

  • 253,000—Chiwerengero cha anthu
  • 1,188—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 19—Mipingo
  • Pa anthu 215 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anayamba Kufesa Mbewu za Ufumu ku Portugal

Kodi anthu anakumana ndi mavuto ati pamene anayamba kulalikira ku Portugal, nanga anathana nawo bwanji?