Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

JW LIBRARY

Mmene Mungaikire JW Library M’chipangizo Chanu Ngati Simukuipeza ku App Store​​—Windows

Mmene Mungaikire JW Library M’chipangizo Chanu Ngati Simukuipeza ku App Store​​—Windows

Ngati simungathe kuika JW Library m’chipangizo chanu chokhala ndi pulogalamu ya Windows pa Windows Store, mukhoza kuika nokha pogwiritsa ntchito mafailo a Windows oikira JW Library.

Lolani chipangizo chanu kuti chiziika mapulogalamu kuchokera kumalo ena: Pitani ku ma Settings > Update & security > For developers. Pamene palembedwa kuti Developer mode, sankhani mbali yakuti “Install apps from any source, including loose files.”

Dawunilodani ndi kulowetsa mafailo a Windows oikira JW Library:

  1. Dinani batani la Dawunilodi patsambali kuti musunge ku local drive mafailo oikira pulogalamuyi.

  2. Pangani Right-click failo yokhala ndi .zip kumapeto kwake kenako mupange unzip.

  3. Tsegulani fodayi, pangani right-click failo yakuti Install.ps1, kenako sankhani Run with PowerShell.

  4. Tsimikizirani kuti mulowetse signing certificate, ngati pakufunikira kutero.

  5. Uthenga wotsimikizira uoneka mukamaliza kulowetsa.

Nthawi ndi nthawi muziona ngati pabwera ma version atsopano apulogalamuyi.

  1. Tsegulani tsamba la ma Settings mu JW Library kuti muone version yatsopano yomwe yaikidwa m’chipangizo chanu.

  2. Ngati nambala ya version yomwe ikuoneka ku ma Settings ili yochepa poyerekezera ndi imene yasonyezedwa m’munsimu, dawunilodani ndi kuika pulogalamuyi potsatira ndondomeko zomwe zafotokozedwa pamwambapa.

Mtundu Wake: 14.3.37 (405633)