NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA January 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila kuyambila pa March 4–April 7, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 1

Gonjetsani Mantha Mwa Kudalila Yehova

Yophunzila mu mlungu wa March 4-10, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 2

Kodi Mwalikonzekela Tsiku Lofunika Kwambili M’caka?

Yophunzila mu mlungu wa March 11-17, 2024.

Kodi Mumacita Zinthu na Akazi Mmene Yehova Amacitila Nawo?

Mosasamala kanthu za cikhalidwe cimene m’bale anakulila, angaphunzile kucita zinthu mwacikondi komanso mwaulemu na akazi monga momwe Yehova amacitila.

Kodi Mudziŵa?

Ni galeta la mtundu wanji limene nduna ya ku Itiyopiya inakwela pamene Filipo anakamba nayo?

NKHANI YOPHUNZILA 3

Yehova Adzakuthandizani m’Nthawi Zovuta

Yophunzila mu mlungu wa March 25-31, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 4

Yehova Amakukonda Kwambili

Yophunzila mu mlungu wa April 1-7, 2024.