Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Palibenso Buku Lothandiza Kwambiri Kuposa Baibulo

Palibenso Buku Lothandiza Kwambiri Kuposa Baibulo

Baibulo ndi buku lomwe limafalitsidwa komanso kumasuliridwa m’zinenero zambiri kuposa buku lina lililonse. Ndiponso mfundo zake zathandiza anthu ambiri kuposa mabuku ena. Mwachitsanzo taganizirani izi:

MABAIBULO OMWE AMASULIRIDWA KOMANSO KUFALITSIDWA

  • 96.5% ya anthu padzikoli ali nalo

  • LIKUPEZEKA m’zinenero 3,350 (LONSE KAPENA MBALI YAKE)

  • 5,000,000,000: Chiwerengero cha mabaibulo amene afalitsidwa. Chiwerengerochi n’choposa mabuku ena onse omwe afalitsidwapo

KUTI MUDZIWE ZAMBIRI

PITANI PAWEBUSAITI YATHU YA JW.ORG. PAWEBUSAITIYI MUKHOZA:

A MBONI ZA YEHOVA AMAKHULUPIRIRA BAIBULO

A MBONI ZA YEHOVA AMADZIPEREKA KUGWIRA NTCHITO YOMASULIRA KOMANSO KUFALITSA BAIBULO.

Pamunsipa pali Mabaibulo omwe takhala tikufalitsa m’mbuyomu.

  • American Standard Version of 1901

  • The Bible in Living English by Byington

  • The Emphatic Diaglott

  • King James Version

  • Revised Standard Version

  • Tischendorf’s New Testament

BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO

  • 180+ Zinenero (LONSE KAPENA MBALI YAKE)

  • 227 MILLION KUCHULUKA KWA MABAIBULO A DZIKO LATSOPANO OMWE AKHALA AKUFALITSIDWA KUCHOKERA MU 1950

Panopa munthu akhoza kuphunzira m’Chingelezi komanso m’Chipwitikizi. Zinenero zina zibwera m’tsogolomu.