Mboni za Yehova Padziko Lonse

Canada

  • Montreal, Canada—Akugawira magazini a Nsanja ya Olonda

Mfundo Zachidule—Canada

  • 38,704,000—Chiwerengero cha anthu
  • 120,388—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,164—Mipingo
  • Pa anthu 325 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada Lagamula Kuti Makhoti Sayenera Kulowerera Dongosolo Lochotsa Munthu Mumpingo

Khoti Lalikulu Kwambiri ku Canada linanena kuti dongosolo lochotsa munthu mumpingo ‘‘si lankhanza koma cholinga chake n’kuthandiza munthuyo kuti abwererenso mumpingo.’’

NTCHITO YOLALIKIRA

Akulalikira Anthu Amitundu Yosiyanasiyana ku Canada

A Mboni za Yehova amalalikira m’zilankhulo zosiyanasiyana n’cholinga choti anthu aphunzire za Mlengi wathu m’chilankhulo chawo.