Pitani ku nkhani yake

Nkhani Zomwe Zangoikidwa Kumene Patsamba Loyamba la Webusaiti Yathu

 

N’chifukwa Chiyani Mulungu Amalola Kuti Anthu Azivutika?

Anthu ambiri amafuna kudziwa kuti n’chifukwa chiyani padzikoli pali mavuto ambiri. Baibulo limapereka yankho logwira mtima pa nkhaniyi.

Kodi Anthu Adzasiya Liti Kumenya Nkhondo?​—Zimene Baibulo Limanena

Posachedwapa nkhondo zonse zidzathetsedwa. Baibulo limafotokoza mmene zimenezi zidzachitikire.

Thandizo la Zaumoyo—Kodi Ufumu wa Mulungu Udzachita Zotani?

Werengani magaziniyi kuti mudziwe zimene Ufumu wa Mulungu udzachite kuti anthufe tidzakhale ndi moyo wathanzi.

Kodi Baibulo Linasinthidwa Kapena Kusokonezedwa?

Popeza kuti Baibulo ndi buku lakalekale, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga wake ndi wolondola mpaka pano?

Kodi Ndi Ndani Amene Adzapulumutse Dzikoli?

Onani zimene ziyenera kusintha komanso mmene zidzasinthire.

 

Kodi Mukudziwa Zotani pa Nkhani ya Malungo?

Mukhoza kudziteteza ngati mumakhala kapena mukupita kudziko limene kuli malungo.

Kodi Anthu 4 Okwera Pamahatchi Akuimira Chiyani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe tanthauzo la ulosi umenewu.

Kodi Aramagedo Idzayambira ku Isiraeli?

Kodi Baibulo limanena zotani?

 

Muzithandiza Ena Polimbana Ndi Maganizo Odziona Kuti Muli Nokhanokha

Malangizo ochokera m’Baibulo angakuthandizeni.

 

Samalani Kuti Musamapusitsike Ndi Nkhani Zabodza

Nkhani zosocheretsa, malipoti abodza ndi mphekesera zafala kwambiri ndipo zingakubweretsereni mavuto.

Kodi Uchigawenga Udzatha?

Kodi Baibulo limanena mfundo zolimbikitsa zotani pa nkhaniyi?

 

Kodi Mawu oti “Msamariya Wachifundo” Amatanthauza Chiyani?

Werengani kuti mudziwe kumene mawu odziwikawa anachokera komanso tanthauzo lake.

Kodi Baibulo Limati Chiyani pa Nkhani ya Isitala?

Werengani kuti mudziwe mmene miyambo 5 imene imachitika pa Isitala inayambira.

Zimene Tingachite Kuti Nsembe ya Yesu Izitithandiza

Onani zinthu ziwiri zofunika kwambiri zimene mungachite.

 

Yesu Adzathetsa Zoipa Zonse

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zimene adzatichitire?

Yesu Adzathetsa Umphawi

Kodi tingasonyeze bwanji kuti timayamikira zimene Yesu watichitira kale ndiponso zimene adzatichitire posachedwapa?

Yesu Adzathetsa Nkhondo

Kodi tingasonyeze bwanji kuyamikira zimene Yesu watichitira kale komanso zomwe adzatichitire posachedwapa?

Ndalama Zambirimbiri Zikuthera Kunkhondo

Kodi Ndi Ndalama Zochuluka Bwanji?

 

Mungakhale ndi Moyo Wosangalala

Magaziniyi ya Galamukani! Ikufotokoza mmene malangizo anzeru a m’Baibulo angakuthandizireni.

 

N’chiyani Chingakuthandizeni Kukhala Ndi Tsogolo Labwino?

Kodi ndi maphunziro, ndalama kapena zinthu zina? Werengani magazini ya Nsanja ya Olonda ino kuti mudziwe zambiri.