Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata Yopita kwa Afilipi

Machaputala

1 2 3 4

Mitu

  • 1

    • Moni (1, 2)

    • Kuthokoza Mulungu; Pemphero la Paulo (3-11)

    • Uthenga wabwino unafalikira kwambiri ngakhale kuti panali mavuto (12-20)

    • Ndikhala ndi moyo kuti ndizitumikira Khristu, ndikamwalira ndipindula (21-26)

    • Makhalidwe anu azigwirizana ndi uthenga wabwino (27-30)

  • 2

    • Akhristu azikhala odzichepetsa (1-4)

    • Kudzichepetsa kwa Khristu komanso kukwezedwa kwake (5-11)

    • Yesetsani kuti mudzapulumuke (12-18)

      • Kuwala ngati zounikira (15)

    • Anatumiza Timoteyo ndi Epafurodito (19-30)

  • 3

    • Sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika (1-11)

      • Zinthu zonse nʼzopanda phindu chifukwa chakuti ndinadziwa Khristu (7-9)

    • Tiyesetse kuti tikalandire mphoto (12-21)

      • Nzika zakumwamba (20)

  • 4

    • Mgwirizano, kusangalala, maganizo abwino (1-9)

      • Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse (6, 7)

    • Anayamikira mphatso zimene Afilipi anapereka (10-20)

    • Moni womaliza (21-23)