Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Uthenga Wabwino Wolembedwa ndi Maliko

Machaputala

1 2 3 4 5 6 7 8 9 10 11 12 13 14 15 16

Mitu

  • 1

    • Yohane Mʼbatizi ankalalikira (1-8)

    • Kubatizidwa kwa Yesu (9-11)

    • Yesu anayesedwa ndi Satana (12, 13)

    • Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (14, 15)

    • Anasankha ophunzira oyambirira (16-20)

    • Anatulutsa mzimu wonyansa (21-28)

    • Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (29-34)

    • Anapemphera kumalo opanda anthu (35-39)

    • Munthu wakhate anachiritsidwa (40-45)

  • 2

    • Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (1-12)

    • Yesu anaitana Levi (13-17)

    • Funso lokhudza kusala kudya (18-22)

    • Yesu ndi ‘Mbuye wa Sabata’ (23-28)

  • 3

    • Munthu wolumala dzanja anachiritsidwa (1-6)

    • Chigulu cha anthu chinali mʼmbali mwa nyanja (7-12)

    • Atumwi 12 (13-19)

    • Kunyoza mzimu woyera (20-30)

    • Mayi komanso azichimwene ake a Yesu (31-35)

  • 4

    • MAFANIZO OKHUDZA UFUMU (1-34)

      • Wofesa mbewu (1-9)

      • Chifukwa chake Yesu ankagwiritsa ntchito mafanizo (10-12)

      • Tanthauzo la fanizo la wofesa mbewu (13-20)

      • Nyale saivindikira ndi dengu (21-23)

      • Muyezo umene mukuyezera (24, 25)

      • Wofesa mbewu amene amagona (26-29)

      • Kanjere ka mpiru (30-32)

      • Anagwiritsa ntchito mafanizo (33, 34)

    • Yesu analetsa mafunde (35-41)

  • 5

    • Yesu anatumiza ziwanda munkhumba (1-20)

    • Mwana wamkazi wa Yairo; mzimayi amene anagwira malaya akunja a Yesu (21-43)

  • 6

    • Yesu anakanidwa mʼdera lakwawo (1-6)

    • Atumwi 12 anapatsidwa malangizo okhudza utumiki (7-13)

    • Imfa ya Yohane Mʼbatizi (14-29)

    • Yesu anadyetsa anthu 5,000 (30-44)

    • Yesu anayenda pamadzi (45-52)

    • Anachiritsa anthu ku Genesareti (53-56)

  • 7

    • Anadzudzula miyambo ya anthu (1-13)

    • Zinthu zimene zimaipitsa munthu zimachokera mumtima (14-23)

    • Chikhulupiriro cha mayi wa Chisurofoinike (24-30)

    • Munthu amene anali ndi vuto losamva anachiritsidwa (31-37)

  • 8

    • Yesu anadyetsa anthu 4,000 (1-9)

    • Anapempha chizindikiro (10-13)

    • Zofufumitsa za Afarisi ndi Herode (14-21)

    • Munthu wavuto losaona anachiritsidwa ku Betsaida (22-26)

    • Petulo anazindikira kuti Yesu ndi Khristu (27-30)

    • Yesu ananeneratu za imfa yake (31-33)

    • Chizindikiro cha wophunzira weniweni (34-38)

  • 9

    • Yesu anasintha maonekedwe ake (1-13)

    • Mnyamata wogwidwa ndi chiwanda anachiritsidwa (14-29)

      • Zinthu zonse ndi zotheka kwa munthu amene ali ndi chikhulupiriro (23)

    • Yesu ananeneratu kachiwiri za imfa yake (30-32)

    • Ophunzira anakangana kuti wamkulu ndi ndani (33-37)

    • Aliyense amene sakulimbana nafe ali kumbali yathu (38-41)

    • Zopunthwitsa (42-48)

    • “Khalani ndi mchere mwa inu nokha” (49, 50)

  • 10

    • Ukwati komanso kutha kwa banja (1-12)

    • Yesu anadalitsa ana (13-16)

    • Funso la munthu wachuma (17-25)

    • Zinthu zimene tikuyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (26-31)

    • Yesu ananeneratunso za imfa yake (32-34)

    • Pempho la Yakobo ndi Yohane (35-45)

      • Yesu anapereka dipo kuti awombole anthu ambiri (45)

    • Batimeyu amene anali ndi vuto losaona anachiritsidwa (46-52)

  • 11

    • Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (1-11)

    • Anatemberera mtengo wamkuyu (12-14)

    • Yesu anayeretsa kachisi (15-18)

    • Zimene tikuphunzira pa mtengo wamkuyu umene unafota (19-26)

    • Anatsutsa ulamuliro wa Yesu (27-33)

  • 12

    • Fanizo la alimi amene anapha anthu (1-12)

    • Mulungu komanso Kaisara (13-17)

    • Funso lokhudza kuuka kwa akufa (18-27)

    • Malamulo awiri aakulu kwambiri (28-34)

    • Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (35-37a)

    • Anawachenjeza kuti asamale ndi alembi (37b-40)

    • Timakobidi tiwiri ta mayi wamasiye wosauka (41-44)

  • 13

    • MAPETO A NTHAWI INO (1-37)

      • Nkhondo, zivomerezi, kusowa kwa chakudya (8)

      • Uthenga wabwino ukuyenera kulalikiridwa (10)

      • Chisautso chachikulu (19)

      • Kubwera kwa Mwana wa munthu (26)

      • Fanizo la mtengo wamkuyu (28-31)

      • Khalani maso (32-37)

  • 14

    • Ansembe anakonza zoti aphe Yesu (1, 2)

    • Anathira Yesu mafuta onunkhira kwambiri (3-9)

    • Yudasi anapereka Yesu (10, 11)

    • Pasika womaliza (12-21)

    • Anayambitsa Mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (22-26)

    • Ananeneratu zoti Petulo adzamukana (27-31)

    • Yesu anapemphera ku Getsemane (32-42)

    • Yesu anagwidwa (43-52)

    • Anaimbidwa mlandu Mʼkhoti Lalikulu la Ayuda (53-65)

    • Petulo anakana Yesu (66-72)

  • 15

    • Yesu anakaonekera pamaso pa Pilato (1-15)

    • Ananyozedwa pagulu (16-20)

    • Anamukhomerera pamtengo ku Gologota (21-32)

    • Imfa ya Yesu (33-41)

    • Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (42-47)

  • 16

    • Yesu anaukitsidwa (1-8)