Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kalata ya Yakobo

Machaputala

1 2 3 4 5

Mitu

  • 1

    • Moni (1)

    • Kupirira kumachititsa kuti tikhale osangalala (2-15)

      • Chikhulupiriro chimakhala cholimba tikamayesedwa (3)

      • Tizipempha ndi chikhulupiriro (5-8)

      • Chilakolako chimabweretsa uchimo ndi imfa (14, 15)

    • Mphatso iliyonse yabwino imachokera kumwamba (16-18)

    • Kumva ndi kuchita zimene mawu akunena (19-25)

      • Munthu amene akudziyangʼanira pagalasi (23, 24)

    • Kulambira koyera komanso kosadetsedwa (26, 27)

  • 2

    • Kuchita zokondera ndi tchimo (1-13)

      • Chikondi ndi lamulo lachifumu (8)

    • Chikhulupiriro chopanda ntchito zake ndi chakufa (14-26)

      • Ziwanda zimakhulupirira ndipo zimanjenjemera (19)

      • Abulahamu ankadziwika kuti ndi mnzake wa Yehova (23)

  • 3

    • Kuweta lilime (1-12)

      • Pasakhale aphunzitsi ambiri (1)

    • Nzeru yochokera kumwamba (13-18)

  • 4

    • Musachite ubwenzi ndi dziko (1-12)

      • Tsutsani Mdyerekezi (7)

      • Yandikirani Mulungu (8)

    • Anawachenjeza kuti apewe kunyada (13-17)

      • “Yehova akalola” (15)

  • 5

    • Anachenjeza anthu achuma (1-6)

    • Mulungu amadalitsa anthu amene amayembekezera moleza mtima (7-11)

    • Mukati “ayi,” azikhaladi ayi (12)

    • Pemphero lachikhulupiriro limagwira ntchito (13-18)

    • Kuthandiza munthu wochimwa kuti abwerere (19, 20)