Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Tisaleke Kulalikila

Tisaleke Kulalikila

Daunilodi:

  1. 1. Mapeto a dziko

    ayandikila ndithu.

    Tilalikile kuti anthu

    akapulumuke.

  2. 2. Tidziŵa zoona

    Sitingacite mantha.

    Tidziŵa M’lungu ali nafe,

    Adzatithandiza.

    (KOLASI)

    Uthenga wabwino

    tiulalikile.

    Inde, Tilalike!

    Monga moto woyaka,

    tiuzeko ena

    Inde, Tilalike!

    Tilalike!

  3. 3. Tigwile mwakhama

    nchitoyi isanathe.

    Tidzayeletsa, inde dzina

    la Yehova M’lungu

    (KOLASI)

    Uthenga wabwino

    tiulalikile

    Inde, Tilalike!

    Monga moto woyaka,

    tiuzeko ena

    Inde, Tilalike!

    Tilalike!

    (BILIJI)

    Tisazimitse cangu, ticite khama

    Tsiku la Yehova silicedwa,

    tisafo’ke!

    (KOLASI)

    Uthenga wabwino

    tiulalikile

    Inde, Tilalike!

    Monga moto woyaka,

    tiuzeko ena

    Inde, Tilalike!

    Tilalike!

    Tilalike!

    Tilalike!